Personal tools
You are here: Home Books Uchi Woyee!

Uchi Woyee!

by Smith Likongwe

Atazizwa ndi ubwino wosiyanasiyana wa uchi, mwana anafuna kudziwa momwe njuchi zimapangira uchi. Amalume ake akufotokoza bwino lomwe za m'gwirizano wa njuchi ndi ukatswiri wakapangidwe ka uchi. Akufotokozanso za ntchito zina za uchi monga kuthandiza pa matenda ena.

After tasting the sweetness of honey, Chifundo is interested to know the honey -making process. Her uncle takes her through the process from nectar collection to the hive and all the intricate operations of the bees up to placement of ripe honey in wax cells. The exciting behaviour of bees is unveiled. The uncle also talks of honey harvesting and health benefits.

 

ISBN 9789996096945 | 32 pages | 210x148 mm | 2022 | Horace Publications, Malawi | Paperback

Categories:

Authors

Editors

Document Actions